-
Machitidwe 11:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Zitatero ndinakumbukira mawu amene Ambuye ankakonda kunena aja akuti, ‘Yohane ankabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+ 17 Choncho ngati Mulungu anawapatsa mphatso yaulere yomwenso anatipatsa ifeyo amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu, ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+
-