Mateyu 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:23 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yesu—Ndi Njira, tsa. 62 Nsanja ya Olonda,4/1/1986, tsa. 21
23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse.