Mateyu 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero, anayendayenda mʼGalileya+ yense ndipo ankaphunzitsa mʼmasunagoge+ mwawo, ankalalikira uthenga wabwino wa Ufumu komanso ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:23 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yesu—Ndi Njira, tsa. 62 Nsanja ya Olonda,4/1/1986, tsa. 21
23 Atatero, anayendayenda mʼGalileya+ yense ndipo ankaphunzitsa mʼmasunagoge+ mwawo, ankalalikira uthenga wabwino wa Ufumu komanso ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+