Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Tamverani kumwamba inu, ndiloleni ndilankhule.Ndipo dziko lapansi limve mawu a pakamwa panga.+ Machitidwe 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+