Salimo 107:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ananena mawu ndipo anawachiritsa,+Moti anawapulumutsa kudzenje la manda.+ Salimo 147:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amatumiza mawu ake+ ndi kusungunula madzi oundanawo.Amachititsa mphepo yake kuwomba,+Ndipo madzi amayenda.
18 Amatumiza mawu ake+ ndi kusungunula madzi oundanawo.Amachititsa mphepo yake kuwomba,+Ndipo madzi amayenda.