Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola kuti ndisapite kudzenje,+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Salimo 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Mulungu adzawombola moyo wanga ku Manda,+Pakuti adzandilandira. [Seʹlah.] Salimo 56:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+ Salimo 103:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+
13 Pakuti inu mwalanditsa moyo wanga ku imfa.+Inu mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe,+Kuti ndiyendeyende pamaso pa Mulungu m’kuwala kumene kumaunikira anthu amoyo.+
4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+