Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndikuitana inu Yehova.+

      Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+

      Kuti musakhale chete pamaso panga,+

      Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+

  • Yesaya 38:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+

      Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+

      Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+

  • Yona 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.

      Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*

      Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena