Yobu 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu amasangalatsidwa naye ndi kunena kuti,‘M’pulumutseni kuti asapite m’dzenje,+Chifukwa ndapeza dipo.*+ Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+ Machitidwe 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+
24 Mulungu amasangalatsidwa naye ndi kunena kuti,‘M’pulumutseni kuti asapite m’dzenje,+Chifukwa ndapeza dipo.*+
17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+
31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+