Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:17 Yandikirani, tsa. 264 Nsanja ya Olonda,7/1/2003, tsa. 18
17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+