Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa mʼManda,*+ Mwandisunga ndi moyo, mwanditeteza kuti ndisatsikire mʼdzenje.*+ Salimo 86:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa chikondi chanu chokhulupirika chimene mumandisonyeza ndi chachikuluNdipo mwapulumutsa moyo wanga ku dzenje la Manda.*+ Yona 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinamira mpaka mʼmunsi mwenimweni mwa mapiri. Zotsekera za dziko lapansi zinayamba kunditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale. Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa mʼdzenje ndili wamoyo.+
3 Inu Yehova, mwanditulutsa mʼManda,*+ Mwandisunga ndi moyo, mwanditeteza kuti ndisatsikire mʼdzenje.*+
13 Chifukwa chikondi chanu chokhulupirika chimene mumandisonyeza ndi chachikuluNdipo mwapulumutsa moyo wanga ku dzenje la Manda.*+
6 Ndinamira mpaka mʼmunsi mwenimweni mwa mapiri. Zotsekera za dziko lapansi zinayamba kunditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale. Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa mʼdzenje ndili wamoyo.+