Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndikuitana inu Yehova.+

      Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+

      Kuti musakhale chete pamaso panga,+

      Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+

  • Salimo 30:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+

      Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+

  • Salimo 86:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+

      Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+

  • Salimo 88:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndakhala womasuka ngati anthu akufa,+

      Ngati anthu ophedwa amene agona m’manda,+

      Anthu amene simukuwakumbukiranso

      Komanso amene sakulandira thandizo kuchokera m’manja mwanu.+

  • Yona 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndinatsikira m’tsinde mwenimweni mwa mapiri.

      Zotsekera za dziko lapansi zinanditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale.*

      Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa m’dzenje ndili wamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena