Salimo 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu Yehova, mwaona zimenezi+ ndipo musakhale chete.+Musakhale patali ndi ine, inu Yehova.+ Salimo 83:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+
83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+