Salimo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndikuitana inu Yehova.+Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+Kuti musakhale chete pamaso panga,+Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+ Salimo 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+ Salimo 83:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+
28 Ndikuitana inu Yehova.+Inu Thanthwe langa, musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana,+Kuti musakhale chete pamaso panga,+Kutinso ine ndisafanane ndi amene akutsikira kudzenje la manda.+
21 Wachita zinthu zonsezi, koma ine ndinakhala chete.+Unali kuganiza kuti ine ndikhala ngati iwe.+Ine ndidzakudzudzula,+ ndipo ndidzaika machimo ako onse poyera iwe ukuona.+
83 Inu Mulungu, musakhale chete.+Musakhale phee osalankhulapo kanthu ndipo musakhale duu osachitapo kanthu, inu Mulungu.+