Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+ Yesaya 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu muzidalira Yehova+ nthawi zonse, pakuti Ya* Yehova ndiye Thanthwe+ mpaka kalekale.
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
9 Ndidzauza Mulungu, thanthwe langa kuti:+“N’chifukwa chiyani mwandiiwala?+Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?”+