Yobu 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye wandiwombola kuti ndisapite kudzenje,+Ndipo moyo wanga udzaona kuwala.’ Salimo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+ Salimo 69:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musalole kuti mtsinje wa madzi othamanga undikokolole,+Kapena kuti madzi akuya andimize,Kapenanso kuti dzenje* lindimeze ndi kutseka pakamwa pake.+ Yesaya 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+
9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+
15 Musalole kuti mtsinje wa madzi othamanga undikokolole,+Kapena kuti madzi akuya andimize,Kapenanso kuti dzenje* lindimeze ndi kutseka pakamwa pake.+
18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+