Numeri 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chotero iwo analowa m’nthaka, limodzi ndi onse amene anali kumbali yawo. Iwo anatsikira ku Manda ali amoyo. Nthakayo inawafotsera,+ moti iwo anafafanizika pakati pa mpingo wonse.+ Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+
33 Chotero iwo analowa m’nthaka, limodzi ndi onse amene anali kumbali yawo. Iwo anatsikira ku Manda ali amoyo. Nthakayo inawafotsera,+ moti iwo anafafanizika pakati pa mpingo wonse.+