Salimo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+ Salimo 88:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi anthu akufa mudzawachitira zodabwitsa?+Kapena kodi anthu akufa, anthu amene sangachite kanthu, adzauka?+Kodi adzakutamandani?+ [Seʹlah.] Salimo 146:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+
9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+
10 Kodi anthu akufa mudzawachitira zodabwitsa?+Kapena kodi anthu akufa, anthu amene sangachite kanthu, adzauka?+Kodi adzakutamandani?+ [Seʹlah.]
4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+