Salimo 88:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi mungachitire zinthu zodabwitsa anthu akufa? Kodi anthu akufa amene sangathe kuchita kanthu angadzuke nʼkukutamandani?+ (Selah)
10 Kodi mungachitire zinthu zodabwitsa anthu akufa? Kodi anthu akufa amene sangathe kuchita kanthu angadzuke nʼkukutamandani?+ (Selah)