Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu akafa, kodi angakhalenso ndi moyo?+

      Ndidzadikira masiku onse a ntchito yanga yokakamiza,

      Mpaka mpumulo wanga utafika.+

  • Salimo 115:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Akufa satamanda Ya,+

      Ngakhalenso aliyense amene amatsikira kulichete.+

  • Yesaya 38:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chifukwa Manda* sangakupatseni ulemerero,+

      Imfa singakutamandeni.+

      Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kuti muwasonyeze kukhulupirika kwanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena