Salimo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa akufa satchula* za inu.Kodi ndi ndani amene angakutamandeni ali mʼManda?*+ Salimo 115:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akufa satamanda Ya,+Ngakhalenso aliyense amene amatsikira kulichete.+