Yobu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye amene moyo+ wa aliyense uli m’dzanja lake,Ndiponso mzimu wa anthu onse.+ Salimo 104:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+ Mlaliki 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+ Mateyu 27:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo Yesu anafuulanso mokweza mawu, kenako anatsirizika.+ Machitidwe 7:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+
29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+
8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+
59 Iwo anapitiriza kumuponya miyala Sitefano, pamene iye anali kuchonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu* wanga.”+