Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . . Aroma 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+