Genesis 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma usadye zipatso za mtengo wodziwitsa chabwino ndi choipa. Chifukwa tsiku limene udzadya, udzafa ndithu.”+ Genesis 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+ Yesaya 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Bambo wako, woyamba uja, anachimwa+ ndipo anthu okulankhulira andilakwira.+
17 Koma usadye zipatso za mtengo wodziwitsa chabwino ndi choipa. Chifukwa tsiku limene udzadya, udzafa ndithu.”+
6 Mkaziyo atamva zimenezo, anayamba kuona kuti zipatso za mtengowo n’zokoma kudya, zokhumbirika ndi zosiririka.+ Choncho anathyola chipatso cha mtengowo n’kudya. Pambuyo pake, anapatsako mwamuna wake pamene anali limodzi, ndipo nayenso anadya.+