Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . . 2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+ 1 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, Adamu sananyengedwe,+ koma mkaziyo ndiye amene ananyengedwa+ ndipo anachimwa.+
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+