Aroma 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira ngati mfumu kuyambira nthawi ya Adamu mpaka ya Mose, ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe ngati mmene anachimwira Adamu, yemwe ndi wofanana ndi amene ankabwera.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:14 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, tsa. 12
14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira ngati mfumu kuyambira nthawi ya Adamu mpaka ya Mose, ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe ngati mmene anachimwira Adamu, yemwe ndi wofanana ndi amene ankabwera.+