Aroma 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:14 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, tsa. 12
14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+