Salimo 89:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kodi pali mwamuna wamphamvu aliyense amene sadzaona imfa?+Kodi angathe kupulumutsa moyo wake m’dzanja la Manda?+ [Seʹlah.] Salimo 104:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+ Salimo 146:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+
48 Kodi pali mwamuna wamphamvu aliyense amene sadzaona imfa?+Kodi angathe kupulumutsa moyo wake m’dzanja la Manda?+ [Seʹlah.]
29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+Ndipo zimabwerera kufumbi.+
4 Mzimu* wake umachoka,+ ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene anali kuganiza zimatheratu.+