Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti ndikudziwa bwino kuti mudzandibwezera ku imfa,+

      Kunyumba yosonkhanako aliyense wamoyo.

  • Salimo 49:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kuti akhale ndi moyo mpaka muyaya osaona dzenje la manda.+

  • Mlaliki 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti ana a anthu ali ndi mapeto, ndipo zinyamanso zili ndi mapeto. Mapeto a zonsezi ndi ofanana.+ Nyama imafa ndipo munthunso amafa.+ Mzimu wa zonsezi ndi umodzi,+ moti munthu saposa nyama, pakuti zonse n’zachabechabe.

  • Mlaliki 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+

  • Aheberi 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mwa chikhulupiriro, Inoki+ anasamutsidwa kuti asafe mozunzika, moti sanapezeke kwina kulikonse chifukwa Mulungu anamusamutsa.+ Pakuti asanasamutsidwe, Mulungu anamuchitira umboni kuti akukondwera naye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena