Yobu 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mwamuna wamphamvu amafa ndipo amagona pansi atagonjetsedwa.Munthu wochokera kufumbi amatha. Kodi ali kuti?+ Salimo 39:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.] Salimo 49:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe munthu wochokera kufumbi, ngakhale atakhala wolemekezeka, sangakhale ndi moyo mpaka kalekale.+Iye amangofanana ndi nyama zimene zaphedwa.+
10 Koma mwamuna wamphamvu amafa ndipo amagona pansi atagonjetsedwa.Munthu wochokera kufumbi amatha. Kodi ali kuti?+
5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.]
12 Komabe munthu wochokera kufumbi, ngakhale atakhala wolemekezeka, sangakhale ndi moyo mpaka kalekale.+Iye amangofanana ndi nyama zimene zaphedwa.+