Salimo 90:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti masiku athu onse atha chifukwa cha mkwiyo wanu.+Zaka zathu zafika kumapeto ngati mpweya wotuluka m’mphuno pousa moyo.+ Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
9 Pakuti masiku athu onse atha chifukwa cha mkwiyo wanu.+Zaka zathu zafika kumapeto ngati mpweya wotuluka m’mphuno pousa moyo.+
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+