Salimo 102:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti masiku a moyo wanga atha ndi kuzimiririka ngati utsi,+Ndipo mafupa anga atentha kwambiri ngati ng’anjo.+ 1 Petulo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+
3 Pakuti masiku a moyo wanga atha ndi kuzimiririka ngati utsi,+Ndipo mafupa anga atentha kwambiri ngati ng’anjo.+
24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+