Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 30:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Khungu langa linakhala lakuda+ ndipo linayoyoka pathupi panga.

      Mafupa anga anatentha chifukwa chouma.

  • Salimo 31:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chifukwa cha chisoni, moyo wanga watha,+

      Ndipo chifukwa cha kuusa moyo kwanga, zaka zanga zafika kumapeto.+

      Chifukwa cha zolakwa zanga, mphamvu zanga zafooka,+

      Ndipo mafupa anga afooka.+

  • Maliro 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iye watumiza moto m’mafupa+ mwanga kuchokera kumwamba, ndipo wafooketsa fupa lililonse.

      Watchera ukonde+ kuti ukole mapazi anga. Wandibweza kumbuyo.

      Wandisandutsa mkazi wosiyidwa popanda thandizo. Ndikudwala tsiku lonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena