Salimo 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene ndinakhala chete osaulula machimo anga, mafupa anga anafooka, chifukwa tsiku lonse ndinali kuvutika mumtima mwanga.+ Salimo 102:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti masiku a moyo wanga atha ndi kuzimiririka ngati utsi,+Ndipo mafupa anga atentha kwambiri ngati ng’anjo.+
3 Pamene ndinakhala chete osaulula machimo anga, mafupa anga anafooka, chifukwa tsiku lonse ndinali kuvutika mumtima mwanga.+
3 Pakuti masiku a moyo wanga atha ndi kuzimiririka ngati utsi,+Ndipo mafupa anga atentha kwambiri ngati ng’anjo.+