Salimo 90:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti kwa inu zaka 1,000 zili ngati dzulo lapitali,+Ndiponso zili ngati ulonda umodzi wa usiku.*+ 2 Petulo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komabe okondedwa, musalephere kuzindikira mfundo imodzi iyi yakuti, tsiku limodzi kwa Yehova* lili ngati zaka 1,000, ndipo zaka 1,000 zili ngati tsiku limodzi.+
8 Komabe okondedwa, musalephere kuzindikira mfundo imodzi iyi yakuti, tsiku limodzi kwa Yehova* lili ngati zaka 1,000, ndipo zaka 1,000 zili ngati tsiku limodzi.+