Salimo 39:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.] Yakobo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzuwa limatuluka ndi kutentha kwake n’kufotetsa zomera, ndipo maluwa a zomerazo amathothoka. Kukongola kwake kumatha. Momwemonso munthu wachuma adzafa akutsatira njira ya moyo wake.+
5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.]
11 Dzuwa limatuluka ndi kutentha kwake n’kufotetsa zomera, ndipo maluwa a zomerazo amathothoka. Kukongola kwake kumatha. Momwemonso munthu wachuma adzafa akutsatira njira ya moyo wake.+