Salimo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu oipa+ adzapita ku Manda,+Ngakhalenso anthu onse a mitundu ina amene aiwala Mulungu.+ Salimo 52:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu adzakupasula kosatha.+Adzakugwetsa ndi kukukokera kunja kwa hema wako,+Ndipo adzakuzula ndithu m’dziko la anthu amoyo.+ [Seʹlah.] Miyambo 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa adzakankhidwa chifukwa cha kuipa kwake,+ koma wolungama adzapeza malo othawirako chifukwa cha mtima wake wosagawanika.+ Yesaya 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,+ ndipo masomphenya anu amene mwaona ndi Manda sadzagwira ntchito.+ Madzi osefukira akadzadutsa+ adzakukokololani.+
5 Mulungu adzakupasula kosatha.+Adzakugwetsa ndi kukukokera kunja kwa hema wako,+Ndipo adzakuzula ndithu m’dziko la anthu amoyo.+ [Seʹlah.]
32 Woipa adzakankhidwa chifukwa cha kuipa kwake,+ koma wolungama adzapeza malo othawirako chifukwa cha mtima wake wosagawanika.+
18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,+ ndipo masomphenya anu amene mwaona ndi Manda sadzagwira ntchito.+ Madzi osefukira akadzadutsa+ adzakukokololani.+