Yesaya 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+
15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+