Yesaya 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa,+Ndipo tachita mgwirizano* ndi Manda.* Madzi osefukira akamadutsa,Safika kuli ife kuno,Chifukwa bodza talisandutsa malo athu othawirakoNdipo tabisala mʼchinyengo.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:15 Nsanja ya Olonda,3/1/2003, ptsa. 13-146/1/1991, ptsa. 16-17 Yesaya 1, tsa. 293
15 Chifukwa anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa,+Ndipo tachita mgwirizano* ndi Manda.* Madzi osefukira akamadutsa,Safika kuli ife kuno,Chifukwa bodza talisandutsa malo athu othawirakoNdipo tabisala mʼchinyengo.”+