Yesaya 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,Ndipo mgwirizano umene mwachita ndi Manda* sudzagwira ntchito.+ Madzi amphamvu osefukira akamadzadutsa,Adzakukokololani.
18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,Ndipo mgwirizano umene mwachita ndi Manda* sudzagwira ntchito.+ Madzi amphamvu osefukira akamadzadutsa,Adzakukokololani.