Yesaya 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa,+Ndipo tachita mgwirizano* ndi Manda.* Madzi osefukira akamadutsa,Safika kuli ife kuno,Chifukwa bodza talisandutsa malo athu othawirakoNdipo tabisala mʼchinyengo.”+
15 Chifukwa anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa,+Ndipo tachita mgwirizano* ndi Manda.* Madzi osefukira akamadutsa,Safika kuli ife kuno,Chifukwa bodza talisandutsa malo athu othawirakoNdipo tabisala mʼchinyengo.”+