Yesaya 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:15 Nsanja ya Olonda,3/1/2003, ptsa. 13-146/1/1991, ptsa. 16-17 Yesaya 1, tsa. 293
15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+