Yesaya 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,+ ndipo masomphenya anu amene mwaona ndi Manda sadzagwira ntchito.+ Madzi osefukira akadzadutsa+ adzakukokololani.+
18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,+ ndipo masomphenya anu amene mwaona ndi Manda sadzagwira ntchito.+ Madzi osefukira akadzadutsa+ adzakukokololani.+