Aroma 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+
14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+