Yesaya 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,Ndipo mgwirizano umene mwachita ndi Manda* sudzagwira ntchito.+ Madzi amphamvu osefukira akamadzadutsa,Adzakukokololani. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:18 Yesaya 1, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 19-20
18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,Ndipo mgwirizano umene mwachita ndi Manda* sudzagwira ntchito.+ Madzi amphamvu osefukira akamadzadutsa,Adzakukokololani.