Yesaya 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,+ ndipo masomphenya anu amene mwaona ndi Manda sadzagwira ntchito.+ Madzi osefukira akadzadutsa+ adzakukokololani.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:18 Yesaya 1, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 19-20
18 Pangano lanu limene mwachita ndi Imfa lidzatha,+ ndipo masomphenya anu amene mwaona ndi Manda sadzagwira ntchito.+ Madzi osefukira akadzadutsa+ adzakukokololani.+