Salimo 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Awatsogolera ku Manda ngati nkhosa zopita kokaphedwa.+Imfa idzakhala m’busa wawo.+Ndipo m’mawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+Matupi awo adzawonongeka.+Aliyense wa iwo malo ake okhala ndi ku Manda, osati malo okwezeka.+
14 Awatsogolera ku Manda ngati nkhosa zopita kokaphedwa.+Imfa idzakhala m’busa wawo.+Ndipo m’mawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+Matupi awo adzawonongeka.+Aliyense wa iwo malo ake okhala ndi ku Manda, osati malo okwezeka.+