Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chilala ndi kutentha zimatenga madzi a chipale chofewa.

      Ndi mmenenso Manda amachitira ndi anthu amene achimwa.+

  • Aroma 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira monga mfumu kuyambira kwa Adamu mpaka kwa Mose,+ ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe monga mmene anachimwira Adamu,+ yemwe ndi wolingana ndi iye amene anali kubwera.+

  • Chivumbulutso 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nditayang’ana, ndinaona hatchi yotuwa. Wokwerapo wake dzina lake anali Imfa. Ndipo Manda+ anali kumutsatira pafupi kwambiri. Iwo anapatsidwa ulamuliro pa gawo limodzi la magawo anayi a dziko lapansi, kuti aphe anthu ndi lupanga lalitali,+ njala,+ mliri wakupha, ndi zilombo+ za padziko lapansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena