Salimo 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Awatsogolera ku Manda ngati nkhosa zopita kokaphedwa.+Imfa idzakhala m’busa wawo.+Ndipo m’mawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+Matupi awo adzawonongeka.+Aliyense wa iwo malo ake okhala ndi ku Manda, osati malo okwezeka.+ Salimo 55:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chiwonongeko chiwagwere!+Atsikire ku Manda ali amoyo.+Pakuti kulikonse kumene apita, zinthu zoipa zimakhala mumtima mwawo.+ Luka 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+
14 Awatsogolera ku Manda ngati nkhosa zopita kokaphedwa.+Imfa idzakhala m’busa wawo.+Ndipo m’mawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+Matupi awo adzawonongeka.+Aliyense wa iwo malo ake okhala ndi ku Manda, osati malo okwezeka.+
15 Chiwonongeko chiwagwere!+Atsikire ku Manda ali amoyo.+Pakuti kulikonse kumene apita, zinthu zoipa zimakhala mumtima mwawo.+
20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+