1 Samueli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ndi Wakupha ndi Wosunga moyo,+Iye ndi Wotsitsira Kumanda,+ ndiponso Woukitsa.+ Yobu 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtambo umafika kumapeto ake n’kutha.Chimodzimodzi ndi munthu amene wapita ku Manda,* sadzabwerako.+
9 Mtambo umafika kumapeto ake n’kutha.Chimodzimodzi ndi munthu amene wapita ku Manda,* sadzabwerako.+