Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndisanapite. Ndikapita sindibweranso,+

      Ndikapita kudziko lamdima wandiweyani,+

  • Yobu 14:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu nawonso amagona pansi osadzuka.+

      Sadzadzuka mpaka kumwamba kutachoka,+

      Sadzadzutsidwa ku tulo tawo.+

  • Salimo 78:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Iye anali kukumbukira nthawi zonse kuti iwo ndi anthu athupi la nyama,+

      Anali kukumbukira kuti moyo wawo umachoka ndipo subwereranso.+

  • Mlaliki 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena